Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 10:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Ndiponso aliyense wosalandira mtengo wake wozunzikirapo* ndi kunditsatira sali woyenera ine.+

  • Yohane 15:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mukanakhala mbali ya dziko, dziko likanakukondani monga mbali yake.+ Koma popeza simuli mbali ya dzikoli,+ koma ine ndinakusankhani kuchokera m’dziko, pa chifukwa chimenechi dziko likudana nanu.+

  • Aroma 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Chotero, ngati tili ana, tilinso olandira cholowa: Olandira cholowa a Mulungu, komanso olandira cholowa anzake+ a Khristu, malinga ngati tivutika+ naye limodzi kuti tikalandire ulemerero limodzi ndi iye.+

  • 1 Atesalonika 3:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiponso pamene tinali nanu limodzi, tinali kukuuziranitu+ kuti tiyenera kudzakumana ndi masautso,+ ndipo mmene zachitikiramu ndi mmenenso inu mukudziwira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena