Mateyu 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Aliyense amene wasiya nyumba, abale, alongo, abambo, amayi, ana kapena minda chifukwa cha dzina langa adzalandira zochuluka kwambiri kuposa zimenezi, ndipo adzapeza moyo wosatha.+ Maliko 10:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 amene panopa sadzapeza zochuluka kuwirikiza maulendo 100+ m’nthawi* ino. Iye adzapeza nyumba, abale, alongo, amayi, ana ndi minda, limodzi ndi mazunzo,+ ndipo m’nthawi imene ikubwerayo, adzapeza moyo wosatha. Chivumbulutso 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usachite mantha ndi mavuto amene ukumane nawo.+ Taona! Mdyerekezi+ adzapitiriza kuponya m’ndende ena a inu, kuti muyesedwe mpaka pamapeto,+ ndipo mudzakhala m’masautso+ masiku 10. Sonyeza kukhulupirika kwako mpaka imfa,+ ndipo ndidzakupatsa mphoto* ya moyo.+
29 Aliyense amene wasiya nyumba, abale, alongo, abambo, amayi, ana kapena minda chifukwa cha dzina langa adzalandira zochuluka kwambiri kuposa zimenezi, ndipo adzapeza moyo wosatha.+
30 amene panopa sadzapeza zochuluka kuwirikiza maulendo 100+ m’nthawi* ino. Iye adzapeza nyumba, abale, alongo, amayi, ana ndi minda, limodzi ndi mazunzo,+ ndipo m’nthawi imene ikubwerayo, adzapeza moyo wosatha.
10 Usachite mantha ndi mavuto amene ukumane nawo.+ Taona! Mdyerekezi+ adzapitiriza kuponya m’ndende ena a inu, kuti muyesedwe mpaka pamapeto,+ ndipo mudzakhala m’masautso+ masiku 10. Sonyeza kukhulupirika kwako mpaka imfa,+ ndipo ndidzakupatsa mphoto* ya moyo.+