Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Moyo wosatha kwa anthu amene popirira m’ntchito yabwino akuyesetsa kupeza ulemerero, ulemu ndi moyo wosakhoza kuwonongeka.+

  • Yakobo 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Wodala ndi munthu wopirira mayesero,+ chifukwa akadzavomerezedwa, adzalandira mphoto* ya moyo,+ umene Yehova analonjeza onse omukonda.+

  • Chivumbulutso 20:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kenako ndinaona mipando yachifumu+ ndi amene anakhalapo. Iwo anapatsidwa mphamvu yoweruza.+ Ndiyeno ndinaona miyoyo ya amene anaphedwa ndi nkhwangwa chifukwa cha kuchitira umboni za Yesu, ndi kulankhula za Mulungu. Ndinaonanso anthu amene sanalambire chilombo+ kapena chifaniziro chake,+ ndipo sanalandire chizindikiro pamphumi pawo ndi padzanja pawo.+ Iwo anakhalanso ndi moyo ndipo analamulira monga mafumu+ limodzi ndi Khristu zaka 1,000.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena