1 Akorinto 15:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Pakuti chokhoza kuwonongekachi chidzavala kusawonongeka,+ ndipo chokhoza kufachi+ chidzavala kusafa. Chivumbulutso 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wodala+ ndi woyera+ ndiye aliyense wouka nawo pa kuuka koyamba. Pa iwo, imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi naye zaka 1,000.+
53 Pakuti chokhoza kuwonongekachi chidzavala kusawonongeka,+ ndipo chokhoza kufachi+ chidzavala kusafa.
6 Wodala+ ndi woyera+ ndiye aliyense wouka nawo pa kuuka koyamba. Pa iwo, imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi naye zaka 1,000.+