Aroma 8:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndani adzatilekanitsa ndi chikondi cha Khristu?+ Chisautso kodi, kapena zowawa, chizunzo, njala, usiwa, zoopsa, kapena lupanga?+ Aheberi 10:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Nthawi zina munali kupirira potonzedwa ndi posautsidwa poyera ngati chionetsero m’bwalo la masewera.+ Ndipo nthawi zina munali kupirira pamene munamva zowawa limodzi ndi ena amene anali kukumana ndi zimenezo.+
35 Ndani adzatilekanitsa ndi chikondi cha Khristu?+ Chisautso kodi, kapena zowawa, chizunzo, njala, usiwa, zoopsa, kapena lupanga?+
33 Nthawi zina munali kupirira potonzedwa ndi posautsidwa poyera ngati chionetsero m’bwalo la masewera.+ Ndipo nthawi zina munali kupirira pamene munamva zowawa limodzi ndi ena amene anali kukumana ndi zimenezo.+