Aroma 8:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndani adzatisiyanitsa ndi chikondi cha Khristu?+ Kodi ndi masautso, zowawa, kuzunzidwa, njala, usiwa, zoopsa kapena lupanga?+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:35 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 59 Nsanja ya Olonda,10/15/2001, tsa. 14
35 Ndani adzatisiyanitsa ndi chikondi cha Khristu?+ Kodi ndi masautso, zowawa, kuzunzidwa, njala, usiwa, zoopsa kapena lupanga?+