Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 13:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndipo mneneri+ kapena wolota malotoyo muzimupha,+ chifukwa walankhula mopandukira Yehova Mulungu wanu amene anakutulutsani m’dziko la Iguputo ndi kukuwombolani m’nyumba yaukapolo. Munthu ameneyo walankhula zimenezo kuti akupatutseni panjira imene Yehova Mulungu wanu anakulamulani kuyendamo.+ Choncho muzichotsa woipayo pakati panu.+

  • Yeremiya 27:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “‘Ine sindinawatume,’ watero Yehova, ‘koma iwo akulosera m’dzina langa monama, ndipo mukawamvera ndidzakubalalitsani.+ Inu pamodzi ndi aneneri amene akulosera kwa inuwo mudzatha.’”+

  • Zekariya 13:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pakadzapezeka munthu aliyense wolosera, bambo ake ndi mayi ake amene anamubereka, adzamuuze kuti, ‘Iwe ufa ndithu, chifukwa walankhula zonama m’dzina la Yehova.’ Ndiyeno bambo ndi mayi akewo adzamulase chifukwa chakuti anali kulosera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena