Numeri 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano Aisiraeli anali kukhala ku Sitimu.+ Ali kumeneko, iwo anayamba kuchita chiwerewere ndi akazi a ku Mowabu.+ 2 Petulo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kuwonjezera apo, ambiri adzatsatira+ khalidwe lotayirira+ la aphunzitsiwo, ndipo chifukwa cha amenewa, anthu adzalankhula monyoza njira ya choonadi.+
25 Tsopano Aisiraeli anali kukhala ku Sitimu.+ Ali kumeneko, iwo anayamba kuchita chiwerewere ndi akazi a ku Mowabu.+
2 Kuwonjezera apo, ambiri adzatsatira+ khalidwe lotayirira+ la aphunzitsiwo, ndipo chifukwa cha amenewa, anthu adzalankhula monyoza njira ya choonadi.+