1 Akorinto 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Musasocheretsedwe. Kugwirizana ndi anthu oipa kumawononga makhalidwe abwino.+ Agalatiya 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munali kuthamanga bwino.+ Anakusokonezani ndani kuti musapitirize kumvera choonadi?+