Deuteronomo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu munaona ndi maso anu zimene Yehova anachita pa nkhani ya Baala wa ku Peori. Yehova Mulungu wanu anawononga pakati panu munthu aliyense amene anatsatira Baala wa ku Peori.+ Yuda 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngakhale kuti mukudziwa kale zonsezi, ndikufuna kukukumbutsani kuti Yehova* atapulumutsa anthu ake powatulutsa mʼdziko la Iguputo,+ pambuyo pake anawononga amene analibe chikhulupiriro.+
3 Inu munaona ndi maso anu zimene Yehova anachita pa nkhani ya Baala wa ku Peori. Yehova Mulungu wanu anawononga pakati panu munthu aliyense amene anatsatira Baala wa ku Peori.+
5 Ngakhale kuti mukudziwa kale zonsezi, ndikufuna kukukumbutsani kuti Yehova* atapulumutsa anthu ake powatulutsa mʼdziko la Iguputo,+ pambuyo pake anawononga amene analibe chikhulupiriro.+