Numeri 14:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ine Yehova ndalankhula. Zimene ndidzachitire gulu lonse la anthu oipali, amene asonkhana kuti atsutsane ndi ine ndi izi: Onse adzafera mʼchipululu muno ndipo adzathera momwe muno.+ 1 Akorinto 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano abale, ndikufuna mudziwe kuti makolo athu akale, onse anali pansi pa mtambo+ ndipo onse anawoloka nyanja.+ 1 Akorinto 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngakhale zinali choncho, ambiri a iwo Mulungu sanakondwere nawo ndipo anaphedwa mʼchipululu.+ Aheberi 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi paja ndi ndani amene anamva koma nʼkupsetsa mtima Mulungu? Kodi si anthu onse amene anatuluka mʼdziko la Iguputo motsogoleredwa ndi Mose?+ Aheberi 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho, tikuona kuti sakanatha kulowa mumpumulowo chifukwa anali opanda chikhulupiriro.+
35 Ine Yehova ndalankhula. Zimene ndidzachitire gulu lonse la anthu oipali, amene asonkhana kuti atsutsane ndi ine ndi izi: Onse adzafera mʼchipululu muno ndipo adzathera momwe muno.+
10 Tsopano abale, ndikufuna mudziwe kuti makolo athu akale, onse anali pansi pa mtambo+ ndipo onse anawoloka nyanja.+
16 Kodi paja ndi ndani amene anamva koma nʼkupsetsa mtima Mulungu? Kodi si anthu onse amene anatuluka mʼdziko la Iguputo motsogoleredwa ndi Mose?+