Ekisodo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Zitatero, Yehova anamukwiyira kwambiri Mose ndipo anati: “Kodi Aroni Mlevi si m’bale wako?+ Ndikudziwa kuti amatha kulankhula. Ndiponso, iye ali m’njira kudzakuchingamira. Akakuona, adzakondwera kwambiri mumtima mwake.+ Salimo 99:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mose ndi Aroni anali pakati pa ansembe ake,+Samueli anali pakati pa anthu amene anali kuitana pa dzina lake.+Iwo anali kuitana Yehova, ndipo iye anali kuwayankha.+ Aheberi 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komanso, munthu amalandira ulemu umenewu, osati mwa kufuna kwake,+ koma mwa kuchita kuitanidwa ndi Mulungu,+ monga mmene anaitanira Aroni.+
14 Zitatero, Yehova anamukwiyira kwambiri Mose ndipo anati: “Kodi Aroni Mlevi si m’bale wako?+ Ndikudziwa kuti amatha kulankhula. Ndiponso, iye ali m’njira kudzakuchingamira. Akakuona, adzakondwera kwambiri mumtima mwake.+
6 Mose ndi Aroni anali pakati pa ansembe ake,+Samueli anali pakati pa anthu amene anali kuitana pa dzina lake.+Iwo anali kuitana Yehova, ndipo iye anali kuwayankha.+
4 Komanso, munthu amalandira ulemu umenewu, osati mwa kufuna kwake,+ koma mwa kuchita kuitanidwa ndi Mulungu,+ monga mmene anaitanira Aroni.+