Genesis 33:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Esau anathamanga kudzakumana naye,+ ndipo anamukumbatira+ ndi kum’psompsona. Atakumbatirana, onse awiri anagwetsa misozi kwambiri. Ekisodo 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Yehova anauza Aroni kuti: “Pita kuchipululu+ kukachingamira Mose.” Chotero Aroni ananyamuka ndipo anakumana ndi Mose paphiri la Mulungu woona,+ nam’psompsona. Machitidwe 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Patapita zaka 40, mngelo anaonekera kwa iye m’malawi a moto pachitsamba chaminga+ m’chipululu, pafupi ndi phiri la Sinai.
4 Esau anathamanga kudzakumana naye,+ ndipo anamukumbatira+ ndi kum’psompsona. Atakumbatirana, onse awiri anagwetsa misozi kwambiri.
27 Kenako Yehova anauza Aroni kuti: “Pita kuchipululu+ kukachingamira Mose.” Chotero Aroni ananyamuka ndipo anakumana ndi Mose paphiri la Mulungu woona,+ nam’psompsona.
30 “Patapita zaka 40, mngelo anaonekera kwa iye m’malawi a moto pachitsamba chaminga+ m’chipululu, pafupi ndi phiri la Sinai.