Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 4:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Aroni ndi ana ake akamaliza kuphimba zinthu za m’malo oyera+ ndi ziwiya zonse+ za m’malo oyerawo posamutsa msasa, ana a Kohati azilowamo n’kudzazinyamula.+ Iwo asamakhudze+ zinthu za m’malo oyerazo chifukwa angafe. Zinthu zimenezi ndizo katundu wa m’chihema chokumanako amene ana a Kohati azinyamula.+

  • Numeri 4:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Azinyamula nsalu za chihema chopatulika+ ndi chihema chokumanako,+ ndiponso chophimba chake,+ chophimba cha chikopa cha katumbu+ chomwe chili pamwamba pake, ndi nsalu yotchinga+ pakhomo la chihema chokumanako.

  • Numeri 4:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Uwu ndiwo utumiki wa mabanja a ana a Merari,+ monga gawo la utumiki wawo m’chihema chokumanako. Itamara mwana wa wansembe Aroni, ndiye aziyang’anira utumiki wawo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena