Numeri 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Aroni azipereka Aleviwo kwa Yehova monga nsembe yoyendetsa uku ndi uku+ yochokera kwa Aisiraeli ndipo iwo azigwira ntchito yotumikira Yehova.+
11 Ndiyeno Aroni azipereka Aleviwo kwa Yehova monga nsembe yoyendetsa uku ndi uku+ yochokera kwa Aisiraeli ndipo iwo azigwira ntchito yotumikira Yehova.+