Levitiko 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Iye azibweretsa yekha mafuta+ pamodzi ndi chidale ngati nsembe yowotcha pamoto yoperekedwa kwa Yehova. Ndipo aziyendetsa zinthu zimenezi uku ndi uku monga nsembe yoyendetsa uku ndi uku+ yoperekedwa kwa Yehova. Numeri 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho Aleviwo anadziyeretsa nʼkuchapa zovala zawo.+ Pambuyo pake, Aroni anawapereka kwa Yehova monga nsembe yoyendetsa uku ndi uku.+ Kenako Aroniyo anawaphimbira machimo awo kuti awayeretse.+
30 Iye azibweretsa yekha mafuta+ pamodzi ndi chidale ngati nsembe yowotcha pamoto yoperekedwa kwa Yehova. Ndipo aziyendetsa zinthu zimenezi uku ndi uku monga nsembe yoyendetsa uku ndi uku+ yoperekedwa kwa Yehova.
21 Choncho Aleviwo anadziyeretsa nʼkuchapa zovala zawo.+ Pambuyo pake, Aroni anawapereka kwa Yehova monga nsembe yoyendetsa uku ndi uku.+ Kenako Aroniyo anawaphimbira machimo awo kuti awayeretse.+