Numeri 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kuti uwayeretse uchite izi: Uwawaze madzi oyeretsera machimo ndipo iwo amete thupi lonse ndi lezala. Komanso achape zovala zawo nʼkudziyeretsa.+
7 Kuti uwayeretse uchite izi: Uwawaze madzi oyeretsera machimo ndipo iwo amete thupi lonse ndi lezala. Komanso achape zovala zawo nʼkudziyeretsa.+