Numeri 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho Aleviwo anadziyeretsa nʼkuchapa zovala zawo.+ Pambuyo pake, Aroni anawapereka kwa Yehova monga nsembe yoyendetsa uku ndi uku.+ Kenako Aroniyo anawaphimbira machimo awo kuti awayeretse.+
21 Choncho Aleviwo anadziyeretsa nʼkuchapa zovala zawo.+ Pambuyo pake, Aroni anawapereka kwa Yehova monga nsembe yoyendetsa uku ndi uku.+ Kenako Aroniyo anawaphimbira machimo awo kuti awayeretse.+