Ekisodo 29:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Zonsezi uziike m’manja mwa Aroni ndi m’manja mwa ana ake,+ ndi kuziweyulira* uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova.+
24 Zonsezi uziike m’manja mwa Aroni ndi m’manja mwa ana ake,+ ndi kuziweyulira* uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova.+