Levitiko 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atatero anaika zonsezi m’manja mwa Aroni ndi m’manja mwa ana ake n’kuyamba kuziweyula* uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova.+
27 Atatero anaika zonsezi m’manja mwa Aroni ndi m’manja mwa ana ake n’kuyamba kuziweyula* uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova.+