Deuteronomo 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Mose analemba Chilamulo+ chimenechi nʼkuchipereka kwa ansembe, omwe ndi Alevi, amene amanyamula likasa la pangano la Yehova, komanso kwa akulu onse a Isiraeli.
9 Kenako Mose analemba Chilamulo+ chimenechi nʼkuchipereka kwa ansembe, omwe ndi Alevi, amene amanyamula likasa la pangano la Yehova, komanso kwa akulu onse a Isiraeli.