Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 37:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mitengo yonyamulirayo anailowetsa m’mphete zam’mbali mwa Likasa zija kuti azinyamulira Likasalo.+

  • Numeri 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Aziliphimbanso ndi zikopa za akatumbu,*+ n’kuyalanso nsalu yabuluu pamwamba pake. Kenako azibwezeretsa mitengo yake yonyamulira.+

  • 2 Mbiri 5:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma mitengo yonyamulirayo inali yaitali, moti nsonga zake zinali kuonekera ku Malo Oyera kutsogolo kwa chipinda chamkati, koma sizinali kuoneka kunja. Mitengo yonyamulirayo ikadali pomwepo mpaka lero.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena