1 Mbiri 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma iwo ananyamulira likasa la Mulungu woonalo pangolo yatsopano+ kuchokera kunyumba ya Abinadabu. Uza ndi Ahiyo+ anali kutsogolera ngoloyo.
7 Koma iwo ananyamulira likasa la Mulungu woonalo pangolo yatsopano+ kuchokera kunyumba ya Abinadabu. Uza ndi Ahiyo+ anali kutsogolera ngoloyo.