1 Mbiri 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma iwo ananyamulira Likasa la Mulungu woonalo pangolo yatsopano+ kuchokera kunyumba ya Abinadabu. Uza ndi Ahiyo ndi amene ankatsogolera ngoloyo.+
7 Koma iwo ananyamulira Likasa la Mulungu woonalo pangolo yatsopano+ kuchokera kunyumba ya Abinadabu. Uza ndi Ahiyo ndi amene ankatsogolera ngoloyo.+