Ekisodo 37:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mitengo yonyamulirayo anailowetsa m’mphete zam’mbali mwa Likasa zija kuti azinyamulira Likasalo.+ 1 Samueli 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho pangani ngolo+ yatsopano, ndipo mutenge ng’ombe ziwiri zoyamwitsa zimene sizinanyamulepo goli+ ndi kuzimangirira kungoloyo. Ana a ng’ombezo muwabweze kunyumba kuti asatsatire amayi awo.
7 Choncho pangani ngolo+ yatsopano, ndipo mutenge ng’ombe ziwiri zoyamwitsa zimene sizinanyamulepo goli+ ndi kuzimangirira kungoloyo. Ana a ng’ombezo muwabweze kunyumba kuti asatsatire amayi awo.