Numeri 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Nali lamulo limene Yehova wapereka. Iye wati, ‘Lankhulani ndi ana a Isiraeli kuti akupatseni ng’ombe yaikazi yofiira, yathanzi. Ng’ombeyo ikhale yopanda chilema+ yomwe sinamangidwepo m’goli chikhalire.+
2 “Nali lamulo limene Yehova wapereka. Iye wati, ‘Lankhulani ndi ana a Isiraeli kuti akupatseni ng’ombe yaikazi yofiira, yathanzi. Ng’ombeyo ikhale yopanda chilema+ yomwe sinamangidwepo m’goli chikhalire.+