2 Samueli 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma iwo anakweza likasa la Mulungu woona pangolo yatsopano+ kuti alichotse kunyumba ya Abinadabu+ imene inali paphiri. Uza ndi Ahiyo,+ ana aamuna a Abinadabu, anali kutsogolera ngolo yatsopanoyo. 1 Mbiri 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma iwo ananyamulira likasa la Mulungu woonalo pangolo yatsopano+ kuchokera kunyumba ya Abinadabu. Uza ndi Ahiyo+ anali kutsogolera ngoloyo.
3 Koma iwo anakweza likasa la Mulungu woona pangolo yatsopano+ kuti alichotse kunyumba ya Abinadabu+ imene inali paphiri. Uza ndi Ahiyo,+ ana aamuna a Abinadabu, anali kutsogolera ngolo yatsopanoyo.
7 Koma iwo ananyamulira likasa la Mulungu woonalo pangolo yatsopano+ kuchokera kunyumba ya Abinadabu. Uza ndi Ahiyo+ anali kutsogolera ngoloyo.