Ekisodo 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye anauza anthuwo kuti: “Pofika tsiku lachitatu mukhale okonzeka. Amuna asagone ndi akazi awo.”*