Ekisodo 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako anauza anthuwo kuti: “Pofika tsiku lachitatu mukhale okonzeka.+ Amunanu musayandikire akazi anu.”*+
15 Kenako anauza anthuwo kuti: “Pofika tsiku lachitatu mukhale okonzeka.+ Amunanu musayandikire akazi anu.”*+