-
Ezekieli 22:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 uli ndi mlandu wa magazi amene wakhetsa+ ndipo wadzidetsa chifukwa cha mafano onyansa amene wapanga.+ Wafupikitsa masiku a moyo wako ndipo zaka zoti ulandire chilango zafika. Choncho ndidzakusandutsa chinthu chotonzedwa pakati pa mitundu ina ya anthu ndiponso ndidzakusandutsa chinthu chimene mayiko onse adzachiseka ndi kuchikuwiza.+
-