Ezekieli 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Iwe mwana wa munthu, ngati dziko landichimwira pochita zosakhulupirika, ine ndidzatambasula dzanja langa nʼkuwononga njira zimene amapezera chakudya.*+ Choncho ndidzatumiza njala mʼdzikolo+ ndipo ndidzapha anthu ndi ziweto.”+
13 “Iwe mwana wa munthu, ngati dziko landichimwira pochita zosakhulupirika, ine ndidzatambasula dzanja langa nʼkuwononga njira zimene amapezera chakudya.*+ Choncho ndidzatumiza njala mʼdzikolo+ ndipo ndidzapha anthu ndi ziweto.”+