-
Ezekieli 47:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
47 Kenako ananditenga n’kupita nanenso kukhomo la Nyumbayo.+ Kumeneko ndinaona madzi+ akutuluka pansi, pakhomo penipeni pa Nyumbayo chakum’mawa,+ pakuti Nyumbayo inayang’ana kum’mawa. Madziwo anali kutuluka pansi n’kumatsetsereka. Anali kutuluka kuchokera kumbali ya kudzanja lamanja kwa Nyumbayo, n’kudutsa kum’mwera kwa guwa lansembe.
-