Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 25:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Yehova ndi wabwino ndi wolungama.+

      N’chifukwa chake amalangiza ochimwa kuti ayende m’njira yoyenera.+

  • Salimo 31:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ubwino wanu,+ umene mwasungira anthu okuopani ndi wochuluka kwambiri!+

      Ubwino umenewu mwapereka kwa anthu othawira kwa inu.

      Mwaupereka kwa iwo, ana a anthu akuona.+

  • Yesaya 63:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndidzanena za ntchito za Yehova zosonyeza kukoma mtima kwake kosatha.+ Ndidzatamanda Yehova, mogwirizana ndi zonse zimene Yehova watichitira.+ Ndidzauza nyumba ya Isiraeli zabwino zochuluka+ zimene iye wawachitira chifukwa cha chifundo chake,+ komanso chifukwa cha kukoma mtima kwake kosatha ndiponso kwakukulu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena