Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 92:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kuti alengeze kuti Yehova ndi wolungama.+

      Iye ndi Thanthwe langa,+ ndipo sachita zosalungama.+

  • Salimo 119:68
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  68 Inu ndinu wabwino ndipo mukuchita zabwino.+

      Ndiphunzitseni malamulo anu.+

  • Salimo 145:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Yehova amakomera mtima aliyense,+

      Ndipo ntchito zake zonse amazichitira chifundo.+

  • Nahumu 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Yehova ndi wabwino+ ndipo ndi malo achitetezo+ pa tsiku la nsautso.+

      Amadziwa amene amathawira kwa iye kuti apeze chitetezo.+

  • Zekariya 9:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ubwino wake ndi waukulu kwambiri+ ndiponso iye ndi wooneka bwino kwambiri.+ Tirigu adzapatsa mphamvu anyamata ndipo vinyo watsopano adzapatsa mphamvu anamwali.”+

  • Machitidwe 14:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Komabe iye sanangokhala wopanda umboni wakuti anachita zabwino.+ Anakupatsani mvula+ kuchokera kumwamba ndi nyengo zimene zokolola zanu zimakhala zambiri. Anadzaza mitima yanu ndi chakudya komanso chimwemwe.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena