Salimo 119:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Inu ndinu wabwino+ ndipo ntchito zanu ndi zabwino. Ndiphunzitseni malamulo anu.+