Salimo 50:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mulungu wawala ali ku Ziyoni,+ mzinda wokongola kwambiri.+ Salimo 90:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ubwino wa Yehova Mulungu wathu ukhale pa ife,+Ndipo mukhazikitse ntchito ya manja athu.+Muidalitse ntchito ya manja athu.+
17 Ubwino wa Yehova Mulungu wathu ukhale pa ife,+Ndipo mukhazikitse ntchito ya manja athu.+Muidalitse ntchito ya manja athu.+