Salimo 68:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mulungu wanu walamula mphamvu zanu kuti zionekere.+Inu Mulungu, sonyezani mphamvu monga mmene mwachitira kwa ife.+ Salimo 118:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Haa! Inu Yehova, chonde tipulumutseni.+Haa! Inu Yehova, chonde tithandizeni kuti zinthu zitiyendere bwino.+ Yesaya 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Yehova, mudzachita chilungamo kuti mutipatse mtendere,+ pakuti ntchito zathu zonse tazikwanitsa chifukwa cha inu.+
28 Mulungu wanu walamula mphamvu zanu kuti zionekere.+Inu Mulungu, sonyezani mphamvu monga mmene mwachitira kwa ife.+
25 Haa! Inu Yehova, chonde tipulumutseni.+Haa! Inu Yehova, chonde tithandizeni kuti zinthu zitiyendere bwino.+
12 Inu Yehova, mudzachita chilungamo kuti mutipatse mtendere,+ pakuti ntchito zathu zonse tazikwanitsa chifukwa cha inu.+