Salimo 42:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Masana Yehova adzalamula kukoma mtima kwake kosatha kuti kufike pa ine,+Ndipo usiku ndidzaimba za iye.+Ndidzapemphera kwa Mulungu wondipatsa moyo.+ Salimo 71:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mukhale thanthwe lachitetezo loti ndizilowamo nthawi zonse.+Lamulani kuti ndipulumutsidwe,+Pakuti inu ndinu thanthwe langa ndi malo anga achitetezo.+ Yesaya 40:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 koma anthu odalira+ Yehova adzapezanso mphamvu.+ Iwo adzaulukira m’mwamba ngati ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Adzathamanga koma osafooka. Adzayenda koma osatopa.”+
8 Masana Yehova adzalamula kukoma mtima kwake kosatha kuti kufike pa ine,+Ndipo usiku ndidzaimba za iye.+Ndidzapemphera kwa Mulungu wondipatsa moyo.+
3 Mukhale thanthwe lachitetezo loti ndizilowamo nthawi zonse.+Lamulani kuti ndipulumutsidwe,+Pakuti inu ndinu thanthwe langa ndi malo anga achitetezo.+
31 koma anthu odalira+ Yehova adzapezanso mphamvu.+ Iwo adzaulukira m’mwamba ngati ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Adzathamanga koma osafooka. Adzayenda koma osatopa.”+