1 Mafumu 18:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Dzanja la Yehova linali ndi Eliya,+ moti iye anakokera chovala chake m’chiuno n’kuchimanga,+ ndipo anayamba kuthamanga n’kupitirira Ahabu mpaka kukafika ku Yezereeli.+ Salimo 84:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mphamvu zawo zidzapitiriza kuwonjezeka pamene akuyenda.+Aliyense wa iwo amaonekera kwa Mulungu mu Ziyoni.+
46 Dzanja la Yehova linali ndi Eliya,+ moti iye anakokera chovala chake m’chiuno n’kuchimanga,+ ndipo anayamba kuthamanga n’kupitirira Ahabu mpaka kukafika ku Yezereeli.+
7 Mphamvu zawo zidzapitiriza kuwonjezeka pamene akuyenda.+Aliyense wa iwo amaonekera kwa Mulungu mu Ziyoni.+