Salimo 138:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova adzakwaniritsa zolinga zimene ali nazo pa ine.+Inu Yehova, kukoma mtima kwanu kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+Musasiye ntchito ya manja anu.+ Aefeso 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano kwa iye amene angathe kuchita zazikulu kwambiri kuposa zonse zimene timapempha kapena kuganiza,+ malinga ndi mphamvu yake imene ikugwira ntchito+ mwa ife,
8 Yehova adzakwaniritsa zolinga zimene ali nazo pa ine.+Inu Yehova, kukoma mtima kwanu kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+Musasiye ntchito ya manja anu.+
20 Tsopano kwa iye amene angathe kuchita zazikulu kwambiri kuposa zonse zimene timapempha kapena kuganiza,+ malinga ndi mphamvu yake imene ikugwira ntchito+ mwa ife,