Salimo 57:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikufuulira Mulungu Wam’mwambamwamba, Mulungu woona amene akuthetsa masoka amenewa kuti zinthu zindiyendere bwino.+ Afilipi 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti ndikutsimikizira kuti iyeyo amene anayambitsa ntchito yabwino kwa inu, adzaipitiriza ndi kuimalizitsa+ m’tsiku+ la Yesu Khristu.
2 Ndikufuulira Mulungu Wam’mwambamwamba, Mulungu woona amene akuthetsa masoka amenewa kuti zinthu zindiyendere bwino.+
6 Pakuti ndikutsimikizira kuti iyeyo amene anayambitsa ntchito yabwino kwa inu, adzaipitiriza ndi kuimalizitsa+ m’tsiku+ la Yesu Khristu.