Salimo 100:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti Yehova ndi wabwino.+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapo mpaka kalekale,+Ndipo kukhulupirika kwake kudzakhalapo ku mibadwomibadwo.+ Salimo 103:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma Yehova adzapitiriza kusonyeza kukoma mtima kwake kosatha mpaka kalekale,+Kwa anthu amene amamuopa.+Ndipo adzapitiriza kusonyeza chilungamo chake kwa ana a ana awo.+
5 Pakuti Yehova ndi wabwino.+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapo mpaka kalekale,+Ndipo kukhulupirika kwake kudzakhalapo ku mibadwomibadwo.+
17 Koma Yehova adzapitiriza kusonyeza kukoma mtima kwake kosatha mpaka kalekale,+Kwa anthu amene amamuopa.+Ndipo adzapitiriza kusonyeza chilungamo chake kwa ana a ana awo.+