Yobu 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Manja anu omwe ndi amene anandiumba, ndipo anandipanga+Kuzungulira thupi langa lonse, koma tsopano mukufuna kundimeza. Yobu 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu mudzaitana ndipo ine ndidzayankha.+Mudzalakalaka ntchito ya manja anu. Salimo 71:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngakhale nditakalamba ndi kumera imvi, inu Mulungu musandisiye,+Kufikira nditanena za dzanja lanu lamphamvu ku m’badwo wotsatira,+Kufikira nditanena za mphamvu zanu kwa onse obwera m’tsogolo.+ 1 Petulo 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho amene akuvutika mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu, aike miyoyo yawo m’manja mwa Mlengi wokhulupirika, pamene akupitiriza kuchita zabwino.+
8 Manja anu omwe ndi amene anandiumba, ndipo anandipanga+Kuzungulira thupi langa lonse, koma tsopano mukufuna kundimeza.
18 Ngakhale nditakalamba ndi kumera imvi, inu Mulungu musandisiye,+Kufikira nditanena za dzanja lanu lamphamvu ku m’badwo wotsatira,+Kufikira nditanena za mphamvu zanu kwa onse obwera m’tsogolo.+
19 Choncho amene akuvutika mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu, aike miyoyo yawo m’manja mwa Mlengi wokhulupirika, pamene akupitiriza kuchita zabwino.+