Salimo 119:73 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 73 Manja anu anandipanga, ndipo anandiumba.+Ndithandizeni kukhala wozindikira, kuti ndiphunzire malamulo anu.+ Salimo 139:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu munapanga impso zanga,+Ndipo munali kunditchinga m’mimba mwa mayi anga.+ Salimo 139:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mafupa anga sanali obisika kwa inu+Pamene munali kundipanga m’malo obisika,+Pamene munali kundiwomba ngati nsalu m’malo apansi kwambiri+ padziko lapansi.
73 Manja anu anandipanga, ndipo anandiumba.+Ndithandizeni kukhala wozindikira, kuti ndiphunzire malamulo anu.+
15 Mafupa anga sanali obisika kwa inu+Pamene munali kundipanga m’malo obisika,+Pamene munali kundiwomba ngati nsalu m’malo apansi kwambiri+ padziko lapansi.