Salimo 119:73 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 73 Manja anu anandipanga komanso kundiumba. Ndithandizeni kuti ndikhale wozindikira,Kuti ndiphunzire malamulo anu.+
73 Manja anu anandipanga komanso kundiumba. Ndithandizeni kuti ndikhale wozindikira,Kuti ndiphunzire malamulo anu.+