Yobu 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Manja anu omwe ndi amene anandiumba, ndipo anandipanga+Kuzungulira thupi langa lonse, koma tsopano mukufuna kundimeza. Salimo 100:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Dziwani kuti Yehova ndi Mulungu.+Iye ndi amene anatipanga, sitinadzipange tokha.+Ndife anthu ake ndi nkhosa zimene akuweta.+ Salimo 138:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova adzakwaniritsa zolinga zimene ali nazo pa ine.+Inu Yehova, kukoma mtima kwanu kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+Musasiye ntchito ya manja anu.+ Salimo 139:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzakutamandani chifukwa munandipanga modabwitsa ndipo zimenezi zimandichititsa mantha.+Ntchito zanu ndi zodabwitsa,+Ndipo ine ndimadziwa bwino zimenezi.+
8 Manja anu omwe ndi amene anandiumba, ndipo anandipanga+Kuzungulira thupi langa lonse, koma tsopano mukufuna kundimeza.
3 Dziwani kuti Yehova ndi Mulungu.+Iye ndi amene anatipanga, sitinadzipange tokha.+Ndife anthu ake ndi nkhosa zimene akuweta.+
8 Yehova adzakwaniritsa zolinga zimene ali nazo pa ine.+Inu Yehova, kukoma mtima kwanu kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+Musasiye ntchito ya manja anu.+
14 Ndidzakutamandani chifukwa munandipanga modabwitsa ndipo zimenezi zimandichititsa mantha.+Ntchito zanu ndi zodabwitsa,+Ndipo ine ndimadziwa bwino zimenezi.+