1 Mafumu 8:66 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Pa tsiku la 8 Solomo anauza anthuwo kuti azipita,+ ndipo anthuwo anadalitsa mfumuyo n’kuyamba kupita kwawo. Anapita akusangalala,+ chimwemwe chitadzaza mumtima,+ chifukwa cha zabwino zonse+ zimene Yehova anachitira Davide mtumiki wake ndi anthu ake Aisiraeli. Salimo 31:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ubwino wanu,+ umene mwasungira anthu okuopani ndi wochuluka kwambiri!+Ubwino umenewu mwapereka kwa anthu othawira kwa inu.Mwaupereka kwa iwo, ana a anthu akuona.+
66 Pa tsiku la 8 Solomo anauza anthuwo kuti azipita,+ ndipo anthuwo anadalitsa mfumuyo n’kuyamba kupita kwawo. Anapita akusangalala,+ chimwemwe chitadzaza mumtima,+ chifukwa cha zabwino zonse+ zimene Yehova anachitira Davide mtumiki wake ndi anthu ake Aisiraeli.
19 Ubwino wanu,+ umene mwasungira anthu okuopani ndi wochuluka kwambiri!+Ubwino umenewu mwapereka kwa anthu othawira kwa inu.Mwaupereka kwa iwo, ana a anthu akuona.+