-
Ezekieli 20:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Pa tsiku limene ndinasankha Isiraeli,+ ndinakweza mkono wanga+ polumbirira mbewu ya nyumba ya Yakobo+ ndi kuwachititsa kuti andidziwe m’dziko la Iguputo.+ Inde, ndinakweza mkono wanga ndi kuwalumbirira kuti, ‘Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’+
-