Salimo 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzaimbira Yehova chifukwa wandifupa ndi zinthu zabwino.+ Salimo 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu Yehova, mukhale wokwezeka mu mphamvu zanu.+Tidzaimba ndi kutamanda mphamvu zanu.+ Salimo 68:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu inu, imbirani Mulungu, muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake.+Muimbireni nyimbo Iye amene akudutsa m’chipululu,+Amene dzina lake ndi Ya,*+ ndipo kondwerani pamaso pake.
4 Anthu inu, imbirani Mulungu, muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake.+Muimbireni nyimbo Iye amene akudutsa m’chipululu,+Amene dzina lake ndi Ya,*+ ndipo kondwerani pamaso pake.