Genesis 48:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mngelo amene wakhala akundiwombola ku masoka anga onse,+ adalitse anyamatawa.+ Dzina langa ndi mayina a makolo anga, Abulahamu ndi Isaki, apitirize kutchulidwa kudzela mwa anawa,+Komanso, anawa adzachulukane, adzakhale khamu la anthu padziko lapansi.”+ 2 Samueli 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma Davide anayankha Rekabu ndi m’bale wake Bana, ana a Rimoni Mbeeroti kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo,+ amene anawombola+ moyo wanga+ m’masautso anga onse,+ Salimo 103:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamanda amene akuwombola moyo wako kudzenje,+Amene akukuveka kukoma mtima kosatha ndi chifundo ngati chisoti chachifumu,+
16 Mngelo amene wakhala akundiwombola ku masoka anga onse,+ adalitse anyamatawa.+ Dzina langa ndi mayina a makolo anga, Abulahamu ndi Isaki, apitirize kutchulidwa kudzela mwa anawa,+Komanso, anawa adzachulukane, adzakhale khamu la anthu padziko lapansi.”+
9 Koma Davide anayankha Rekabu ndi m’bale wake Bana, ana a Rimoni Mbeeroti kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo,+ amene anawombola+ moyo wanga+ m’masautso anga onse,+
4 Tamanda amene akuwombola moyo wako kudzenje,+Amene akukuveka kukoma mtima kosatha ndi chifundo ngati chisoti chachifumu,+